Malire a Kuchotsa Ndalama

Malire a Kuchotsa Ndalama

Malire a kuchotsa ndalama pa 888bets amathandiza kuteteza ndalama zanu. Malireni amasiyana ngati mwatsimikizidwa kapena ayi.

Malire a Kuchotsa Ndalama:

Mtundu wa WogwiritsaPa nthawi iliyonseKuchotsa Max/tsikuMalire a Tsiku
OsatsimikizidwaOsachepera K50 – K150,0005 ma withdrawalK150,000 pa tsiku
OtsimikizidwaOsachepera K50 – K750,0005 ma withdrawalK3,000,000 pa tsiku

Zofunika Kuzidziwa:

  • Simungathe kuchotsa kuposa zomwe muli nazo.

  • Kuchotsa sikuloledwa kupitirira 5 pa 24 hours.

  • Muyenera kuchita deposit koyamba musanachotse.

  • Malire amasinthidwa tsiku ndi tsiku.

    • Related Articles

    • Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri pa Kuyika ndi Kuchotsa Ndalama kudzera mu Banki

      1. Ndingayike bwanji ndalama kudzera mu banki? Dinani Deposit, sankhani Bank, lembani ndalama, pezani tsatanetsatane wa banki, kenako sambutsani pogwiritsa ntchito app, USSD kapena internet banking. 2. Kodi ndingachotse ku mobile money ngati ...
    • MALIRE, BONASI NDI ZOLOWEDWA ZA PROMOSHONI

      888bets Malawi imakonda kupatsa makasitomala mphotho, koma bonasi iliyonse imatsatiridwa ndi malamulo oti zinthu zikhale zoyenera kwa aliyense. Werengani malangizo awa musanalandire kapena kugwiritsa ntchito bonasi iliyonse. 1. Malamulo a Promoshoni ...
    • Malire a Kuyika Ndalama

      88bets imayika malire pa kuyika ndalama kutengera ngati mwatsimikizidwa (KYC) kapena ayi. Malire a Kuyika Ndalama: Mtundu wa Wogwiritsa Pa nthawi iliyonse Malire a Tsiku Osatsimikizidwa Osachepera K50 – K500,000 K1,000,000 pa tsiku Otsimikizidwa ...
    • 🇲🇼 Ndingapambane Ndalama Zingati pa Aviator?

      Ku 888bets Malawi, masewera a Aviator amapatsa osewera mwayi wopambana ndalama zambiri kuchokera ku ndalama zochepa—ndichifukwa chake ndi amodzi mwa masewera otchuka kwambiri. ? Zomwe Mumapambana = Kubetcha × Multiplier Kuchuluka kwa ndalama zimene ...
    • Momwe Mungachotsere Ndalama ku Akaunti Ya Banki?

      Kuchotsa ndalama kuchokera ku akaunti ya 888bets kupita ku banki yanu ndi kophweka komanso kwachangu. Tsatirani izi: Lowani mu akaunti yanu ya 888bets. Dinani pa balance yomwe ili pakona yakumanja pa tsamba. Sankhani Withdraw. Sankhani Bank ngati ...